Levitiko 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni kuti, ‘Aliyense wa inu asadzidetse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.+ Levitiko 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Asamamete mpala mitu yawo,+ asamamete ndevu zamʼmasaya mwawo ndipo asamadzitemeteme thupi lawo.+
21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni kuti, ‘Aliyense wa inu asadzidetse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.+