Levitiko 11:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uzani Aisiraeli kuti, ‘Zamoyo zapadziko lapansi* zimene mungadye+ ndi izi: 3 Mungadye nyama iliyonse imene ili ndi ziboda zogawanika zokhala ndi mpata pakati, yomwenso imabzikula.
2 “Uzani Aisiraeli kuti, ‘Zamoyo zapadziko lapansi* zimene mungadye+ ndi izi: 3 Mungadye nyama iliyonse imene ili ndi ziboda zogawanika zokhala ndi mpata pakati, yomwenso imabzikula.