15 Ngati mʼbale kapena mlongo alibe zovala komanso chakudya chokwanira pa tsikulo, 16 koma wina mwa inu nʼkumuuza kuti, “Uyende bwino, upeze zovala ndi zakudya za tsiku lililonse,” koma osamupatsa zimene akufunikirazo kuti akhale ndi moyo, kodi pali phindu lanji?+