Deuteronomo 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Pamene ndinkakutsogolerani kwa zaka 40 mʼchipululu,+ zovala zanu sizinathe ndiponso nsapato zanu sizinathe kumapazi anu.+ Nehemiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kwa zaka 40 munawapatsa chakudya mʼchipululu+ moti sanasowe kanthu. Zovala zawo sizinathe+ ndipo mapazi awo sanatupe. Salimo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova ndi Mʼbusa wanga.+ Sindidzasowa kanthu.+ Salimo 34:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Opani Yehova, inu oyera ake onse,Chifukwa onse amene amamuopa sasowa kanthu.+ כ [Kaph] 10 Ngakhale mikango yamphamvu* ingakhale ndi njala chifukwa chosowa chakudya.Koma anthu amene akufunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+
5 ‘Pamene ndinkakutsogolerani kwa zaka 40 mʼchipululu,+ zovala zanu sizinathe ndiponso nsapato zanu sizinathe kumapazi anu.+
21 Kwa zaka 40 munawapatsa chakudya mʼchipululu+ moti sanasowe kanthu. Zovala zawo sizinathe+ ndipo mapazi awo sanatupe.
9 Opani Yehova, inu oyera ake onse,Chifukwa onse amene amamuopa sasowa kanthu.+ כ [Kaph] 10 Ngakhale mikango yamphamvu* ingakhale ndi njala chifukwa chosowa chakudya.Koma anthu amene akufunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+