Deuteronomo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwamuna akakwatira kumene, asamakhale mʼgulu lankhondo, ndiponso asamapatsidwe ntchito iliyonse. Azikhala kunyumba kwa chaka chimodzi osachita zinthu zimenezi kuti asangalatse mkazi wake.+
5 Mwamuna akakwatira kumene, asamakhale mʼgulu lankhondo, ndiponso asamapatsidwe ntchito iliyonse. Azikhala kunyumba kwa chaka chimodzi osachita zinthu zimenezi kuti asangalatse mkazi wake.+