Miyambo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amanyasidwa ndi masikelo achinyengo,Koma sikelo imene imayeza molondola imamusangalatsa.*+ Miyambo 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyala yachinyengo yoyezera komanso miyezo yachinyengo,*Zonsezi nʼzonyansa kwa Yehova.+ Mika 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi ndingakhale woyera* ndili ndi sikelo yachinyengo,Ndiponso thumba la miyala yachinyengo yoyezera zinthu?+
11 Kodi ndingakhale woyera* ndili ndi sikelo yachinyengo,Ndiponso thumba la miyala yachinyengo yoyezera zinthu?+