-
Yoswa 13:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako Mose anagawira cholowa fuko la Rubeni motsatira mabanja awo.
-
-
Yoswa 21:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Kademoti ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Mefaata ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.
-