Deuteronomo 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukayandikira mzinda kuti mumenyane nawo, muzilengeza kwa anthu amumzindawo mfundo za mtendere.+