Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa nthawi imeneyo tinatenga dzikoli kukhala lathu kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼchigwa cha Arinoni* ndi hafu ya dera lamapiri la Giliyadi. Ndipo ndinapereka mizinda yake kwa fuko la Rubeni ndi fuko la Gadi.+

  • Deuteronomo 4:47, 48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Iwo anamulanda dziko lakelo komanso dziko la Ogi+ mfumu ya Basana. Amenewa ndi mafumu awiri a Aamori amene anali kuchigawo chakumʼmawa kwa Yorodano. 48 Dera limeneli linayambira ku Aroweli+ mʼmphepete mwa chigwa cha Arinoni* mpaka kuphiri la Sione, limene ndi phiri la Herimoni,+

  • Yoswa 13:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa fuko la Rubeni ndi kwa fuko la Gadi, kutsidya lakumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano.+ 9 Cholowa chawo chinayambira kumzinda wa Aroweli+ umene uli mʼmbali mwa chigwa cha Arinoni,+ ndiponso mzinda umene uli pakatikati pa chigwacho, kuphatikizapo malo onse okwera a Medeba mpaka kukafika ku Diboni.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena