Deuteronomo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mafuko a Rubeni ndi Gadi+ ndinawapatsa dera lochokera ku Giliyadi kukafika kuchigwa cha Arinoni,* ndipo malire anali pakati pa chigwacho. Dera limeneli linakafikanso kuchigwa cha Yaboki, amene ndi malire a Aamoni. Oweruza 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kukanena kuti: “Yefita wanena kuti: ‘Aisiraeli sanatenge dziko la Mowabu+ ndi dziko la Aamoni+
16 Mafuko a Rubeni ndi Gadi+ ndinawapatsa dera lochokera ku Giliyadi kukafika kuchigwa cha Arinoni,* ndipo malire anali pakati pa chigwacho. Dera limeneli linakafikanso kuchigwa cha Yaboki, amene ndi malire a Aamoni.