Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 ndiyeno iwo nʼkuzindikira kulakwa kwawo mʼdziko limene anawatengeralo+ nʼkulapa,+ ndiponso akapempha chifundo kwa inu mʼdziko la adani awowo+ nʼkunena kuti, ‘Tachimwa, talakwitsa ndiponso tachita zinthu zoipa,’+

  • Nehemiya 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma mukadzabwerera kwa ine nʼkumatsatira malamulo anga, ngakhale anthu a mtundu wanu atamwazikira kumalekezero akumwamba, ndidzawasonkhanitsa+ kuchokera kumeneko nʼkuwabweretsa kumalo amene ndasankha kuti kukhale dzina langa.’+

  • Ezekieli 18:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Munthu woipayo akazindikira kuti zimene akuchita ndi zoipa nʼkusiya kuchita zoipazo, ndithu iye adzapitiriza kukhala ndi moyo. Sadzafa ayi.

  • Yoweli 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ngʼambani mitima yanu,+ osati zovala zanu,+

      Ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu,

      Chifukwa iye ndi wachifundo, wokoma mtima, wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka.+

      Iye adzasintha maganizo okubweretserani tsoka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena