-
Yoswa 12:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Yoswa ndi Aisiraeli anagonjetsa mafumu akudera lakumadzulo kwa mtsinje wa Yorodano, kuchokera ku Baala-gadi+ kuchigwa cha Lebanoni+ mpaka kuphiri la Halaki,+ limene lili moyangʼanizana ndi Seiri.+ Atawagonjetsa, Yoswa anapereka dzikolo kwa mafuko a Isiraeli poligawa mʼmagawomagawo.+ 8 Dzikoli linkaphatikizapo dera lamapiri, dera la Sefela, chigwa cha Araba, malo otsetsereka, chipululu ndi Negebu.+ Limeneli linali dziko la Ahiti, Aamori,+ Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+ Mafumu awo anali awa:
-