Yoswa 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 anachita mantha kwambiri+ chifukwa Gibiyoni unali mzinda waukulu ngati mzinda wolamulidwa ndi mfumu. Komanso mzindawo unali waukulu kuposa mzinda wa Ai,+ ndipo amuna onse akumeneko anali asilikali. Yoswa 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Panalibe mzinda winanso umene unagwirizana za mtendere ndi Aisiraeli, kupatulapo Ahivi a ku Gibiyoni.+ Aisiraeli anamenyana ndi mizinda ina yonse nʼkuigonjetsa.+
2 anachita mantha kwambiri+ chifukwa Gibiyoni unali mzinda waukulu ngati mzinda wolamulidwa ndi mfumu. Komanso mzindawo unali waukulu kuposa mzinda wa Ai,+ ndipo amuna onse akumeneko anali asilikali.
19 Panalibe mzinda winanso umene unagwirizana za mtendere ndi Aisiraeli, kupatulapo Ahivi a ku Gibiyoni.+ Aisiraeli anamenyana ndi mizinda ina yonse nʼkuigonjetsa.+