-
Yoswa 9:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho anachita zinthu mwanzeru. Anaika chakudya mʼmatumba akutha nʼkukweza pa abulu. Ananyamulanso vinyo mʼmatumba achikopa akutha, atawasoka mongʼambika.
-