-
Yoswa 9:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Atsogoleriwo ananenanso kuti: “Asaphedwe, koma azitola nkhuni ndiponso kutungira madzi gulu lonse la Aisiraeli.” Izi ndi zimene atsogoleriwo anawalonjeza.
-