Numeri 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Upereke malangizo awa kwa Aisiraeli: ‘Awa ndi malire a dziko la Kanani, dziko limene ndidzakupatseni kuti likhale cholowa chanu.+ Numeri 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchokera kuphiri la Hora, mukalembe malirewo mpaka kukafika ku Lebo-hamati,*+ ndipo malirewo akathere ku Zedadi.+
2 “Upereke malangizo awa kwa Aisiraeli: ‘Awa ndi malire a dziko la Kanani, dziko limene ndidzakupatseni kuti likhale cholowa chanu.+
8 Kuchokera kuphiri la Hora, mukalembe malirewo mpaka kukafika ku Lebo-hamati,*+ ndipo malirewo akathere ku Zedadi.+