Yoswa 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maere oyamba anagwera fuko la Benjamini motsatira mabanja awo, ndipo anapatsidwa dera limene linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+ Yoswa 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Malirewo anapitirira kukafika kumʼmwera kwa malo otsetsereka otchedwa Luzi, kutanthauza Beteli.+ Kuchokera ku Luzi anatsetserekera ku Ataroti-adara,+ nʼkukadutsa paphiri lakumʼmwera kwa Beti-horoni Wakumunsi.+
11 Maere oyamba anagwera fuko la Benjamini motsatira mabanja awo, ndipo anapatsidwa dera limene linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+
13 Malirewo anapitirira kukafika kumʼmwera kwa malo otsetsereka otchedwa Luzi, kutanthauza Beteli.+ Kuchokera ku Luzi anatsetserekera ku Ataroti-adara,+ nʼkukadutsa paphiri lakumʼmwera kwa Beti-horoni Wakumunsi.+