Yoswa 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mizinda ya kumapeto kwa gawo la fuko la Yuda, chakumalire ndi Edomu+ kumʼmwera, inali Kabizeeli, Ederi, Yaguri, Yoswa 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Zikilaga,+ Madimana, Sanasana, 1 Samueli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho pa tsikuli Akisi anapatsa Davide mzinda wa Zikilaga.+ Nʼchifukwa chake mzinda wa Zikilaga ndi wa mafumu a Yuda mpaka lero.
21 Mizinda ya kumapeto kwa gawo la fuko la Yuda, chakumalire ndi Edomu+ kumʼmwera, inali Kabizeeli, Ederi, Yaguri,
6 Choncho pa tsikuli Akisi anapatsa Davide mzinda wa Zikilaga.+ Nʼchifukwa chake mzinda wa Zikilaga ndi wa mafumu a Yuda mpaka lero.