2 Samueli 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo anatumiza anthu kwa Davide. Anatumizanso matabwa a mkungudza,+ akalipentala komanso anthu oswa miyala yomangira makoma ndipo anayamba kumanga nyumba* ya Davide.+ 1 Mafumu 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Hiramu, mfumu ya ku Turo,+ atamva kuti Solomo wadzozedwa kukhala mfumu mʼmalo mwa bambo ake, anatuma atumiki ake kuti apite kwa Solomo popeza Hiramuyo anali mnzake wa Davide.+
11 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo anatumiza anthu kwa Davide. Anatumizanso matabwa a mkungudza,+ akalipentala komanso anthu oswa miyala yomangira makoma ndipo anayamba kumanga nyumba* ya Davide.+
5 Hiramu, mfumu ya ku Turo,+ atamva kuti Solomo wadzozedwa kukhala mfumu mʼmalo mwa bambo ake, anatuma atumiki ake kuti apite kwa Solomo popeza Hiramuyo anali mnzake wa Davide.+