Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 11:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pambuyo pake, Harana anamwalira mumzinda wa Uri+ womwe ndi wa Akasidi,+ kumene anabadwira. Anamwalira bambo ake Tera ali ndi moyo.

  • Genesis 11:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako Tera anatenga mwana wake Abulamu, mdzukulu+ wake Loti mwana wa Harana ndi Sarai mpongozi wake, mkazi wa mwana wake Abulamu, nʼkuchoka mumzinda wa Uri womwe ndi wa Akasidi kupita kudziko la Kanani.+ Patapita nthawi anafika ku Harana+ ndipo anayamba kukhala kumeneko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena