Ekisodo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Patsala mliri umodzi wokha woti ndigwetsere Farao ndi Iguputo. Kenako adzakulolani kuchoka mʼdziko lino.+ Pokuuzani kuti muchoke, adzachita kukuthamangitsani.+
11 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Patsala mliri umodzi wokha woti ndigwetsere Farao ndi Iguputo. Kenako adzakulolani kuchoka mʼdziko lino.+ Pokuuzani kuti muchoke, adzachita kukuthamangitsani.+