Ekisodo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aiguputo ankawathamangira,+ ndipo magaleta onse a Farao, asilikali apamahatchi ndi gulu lake lankhondo anawayandikira. Aisiraeliwo anali atamanga msasa mʼmphepete mwa nyanja, pafupi ndi Pihahiroti moyangʼanizana ndi Baala-zefoni.
9 Aiguputo ankawathamangira,+ ndipo magaleta onse a Farao, asilikali apamahatchi ndi gulu lake lankhondo anawayandikira. Aisiraeliwo anali atamanga msasa mʼmphepete mwa nyanja, pafupi ndi Pihahiroti moyangʼanizana ndi Baala-zefoni.