Nehemiya 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munawapatsa maufumu ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo mʼzigawozigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ lomwe ndi dziko la mfumu ya Hesiboni+ komanso dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.
22 Munawapatsa maufumu ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo mʼzigawozigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ lomwe ndi dziko la mfumu ya Hesiboni+ komanso dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.