Levitiko 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho asamaperekenso nsembe zawo kwa ziwanda zooneka ngati mbuzi+ zimene akuzilambira.*+ Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale, mʼmibadwo yanu yonse.”’ Ezekieli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sanasiye uhule umene ankachita ali ku Iguputo. Aiguputowo ankagona naye kuyambira ali kamtsikana. Iwo ankasisita pamtima pake ali namwali ndipo ankachita naye zachiwerewere.+
7 Choncho asamaperekenso nsembe zawo kwa ziwanda zooneka ngati mbuzi+ zimene akuzilambira.*+ Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale, mʼmibadwo yanu yonse.”’
8 Iye sanasiye uhule umene ankachita ali ku Iguputo. Aiguputowo ankagona naye kuyambira ali kamtsikana. Iwo ankasisita pamtima pake ali namwali ndipo ankachita naye zachiwerewere.+