Oweruza 2:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Yoswa, mtumiki wa Yehova, mwana wa Nuni, anamwalira ali ndi zaka 110.+ 9 Ndipo anamuika mʼmanda ku Timinati-heresi,+ mʼdera limene analandira monga cholowa chake, mʼdera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+
8 Kenako Yoswa, mtumiki wa Yehova, mwana wa Nuni, anamwalira ali ndi zaka 110.+ 9 Ndipo anamuika mʼmanda ku Timinati-heresi,+ mʼdera limene analandira monga cholowa chake, mʼdera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+