-
Deuteronomo 31:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo amene akukhala mʼmizinda yanu,* kuti amvetsere komanso kuti aphunzire zokhudza Yehova Mulungu wanu, kuti azimuopa ndiponso kuti azitsatira mosamala mawu onse a mʼChilamulo ichi. 13 Akatero ana awo amene sakudziwa Chilamulo ichi adzamvetsera+ ndipo adzaphunzira kuopa Yehova Mulungu wanu, masiku onse amene mudzakhale mʼdziko limene mukuwoloka Yorodano kukalitenga kuti likhale lanu.”+
-