Oweruza 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amidiyani ndi Aamaleki pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa+ anadzaza mʼchigwa chonse chifukwa anali ambiri ngati dzombe. Ngamila zawo zinali zosawerengeka,+ zambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.
12 Amidiyani ndi Aamaleki pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa+ anadzaza mʼchigwa chonse chifukwa anali ambiri ngati dzombe. Ngamila zawo zinali zosawerengeka,+ zambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.