Oweruza 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Aisiraeli sankamvera oweruzawo. Iwo ankachita chiwerewere ndi milungu ina ndi kuigwadira. Anasiya mwamsanga njira imene makolo awo anayendamo. Makolo awo ankamvera malamulo a Yehova,+ koma iwo sanachite zimenezo.
17 Koma Aisiraeli sankamvera oweruzawo. Iwo ankachita chiwerewere ndi milungu ina ndi kuigwadira. Anasiya mwamsanga njira imene makolo awo anayendamo. Makolo awo ankamvera malamulo a Yehova,+ koma iwo sanachite zimenezo.