Salimo 106:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi zambiri ankawapulumutsa,+Koma iwo ankamupandukira komanso sankamvera,+Ndipo ankawonongedwa chifukwa cha zolakwa zawo.+
43 Nthawi zambiri ankawapulumutsa,+Koma iwo ankamupandukira komanso sankamvera,+Ndipo ankawonongedwa chifukwa cha zolakwa zawo.+