Rute 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale kuti ndinedi wokuwombolani,+ koma pali wachibale wina wapafupi kwambiri kuposa ine amene angakuwombole.+
12 Ngakhale kuti ndinedi wokuwombolani,+ koma pali wachibale wina wapafupi kwambiri kuposa ine amene angakuwombole.+