1 Samueli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye Yehova anauza Samueli kuti: “Tamvera! Ndichita zinazake mu Isiraeli zoti munthu aliyense akadzamva mʼmakutu ake onse mudzalira.+
11 Ndiye Yehova anauza Samueli kuti: “Tamvera! Ndichita zinazake mu Isiraeli zoti munthu aliyense akadzamva mʼmakutu ake onse mudzalira.+