Numeri 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Masiku onse a lonjezo lake lokhala Mnaziri, lezala lisamadutse mʼmutu wake.+ Azikhala woyera posiya tsitsi lakumutu kwake kuti likule mpaka masiku amene anadzipereka kwa Yehova atatha.
5 Masiku onse a lonjezo lake lokhala Mnaziri, lezala lisamadutse mʼmutu wake.+ Azikhala woyera posiya tsitsi lakumutu kwake kuti likule mpaka masiku amene anadzipereka kwa Yehova atatha.