Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba, anadziwa kuti Samueli ndi amene wasankhidwa kukhala mneneri wa Yehova.

  • 1 Samueli 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakupulumutsani kwa adani anu onse okuzungulirani kuti mukhale pa mtendere.+

  • 1 Samueli 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Patapita nthawi, Samueli+ anamwalira. Aisiraeli onse anasonkhana kuti alire maliro ake ndipo anamuika mʼmanda kunyumba kwake ku Rama.+ Kenako Davide ananyamuka nʼkupita kuchipululu cha Parana.

  • Machitidwe 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Zonsezi zinachitika mʼzaka pafupifupi 450.

      Zimenezi zitatha anawapatsa oweruza mpaka kudzafika pa nthawi ya mneneri Samueli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena