Ekisodo 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mukamandipangira guwa lansembe lamiyala, musamamangire miyala yosemedwa ndi zida.+ Chifukwa mukagwiritsa ntchito miyala yosema, ndiye kuti mwadetsa guwalo.
25 Mukamandipangira guwa lansembe lamiyala, musamamangire miyala yosemedwa ndi zida.+ Chifukwa mukagwiritsa ntchito miyala yosema, ndiye kuti mwadetsa guwalo.