1 Samueli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno abulu* a Kisi atasowa, Kisi anauza mwana wake Sauli kuti: “Tenga wantchito mmodzi ndipo mupite mukafunefune abulu.” 1 Samueli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika mʼdera la Zufi, Sauli anauza wantchito wake uja kuti: “Tiye tibwerere kunyumba, chifukwa bambo anga angasiye kuganizira za abulu nʼkuyamba kutidera nkhawa ifeyo.”+
3 Ndiyeno abulu* a Kisi atasowa, Kisi anauza mwana wake Sauli kuti: “Tenga wantchito mmodzi ndipo mupite mukafunefune abulu.”
5 Atafika mʼdera la Zufi, Sauli anauza wantchito wake uja kuti: “Tiye tibwerere kunyumba, chifukwa bambo anga angasiye kuganizira za abulu nʼkuyamba kutidera nkhawa ifeyo.”+