1 Samueli 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sauli ndi mtumiki wake ananyamuka kupita kuphiri kuja. Kumeneko anakumana ndi kagulu ka aneneri. Nthawi yomweyo, mzimu wa Mulungu unamʼpatsa mphamvu+ ndipo nayenso anayamba kulosera.+
10 Sauli ndi mtumiki wake ananyamuka kupita kuphiri kuja. Kumeneko anakumana ndi kagulu ka aneneri. Nthawi yomweyo, mzimu wa Mulungu unamʼpatsa mphamvu+ ndipo nayenso anayamba kulosera.+