1 Samueli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno abulu* a Kisi atasowa, Kisi anauza mwana wake Sauli kuti: “Tenga wantchito mmodzi ndipo mupite mukafunefune abulu.”
3 Ndiyeno abulu* a Kisi atasowa, Kisi anauza mwana wake Sauli kuti: “Tenga wantchito mmodzi ndipo mupite mukafunefune abulu.”