1 Samueli 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anthu anauza Samueli kuti: “Amene ankanena kuti, ‘Sauli sangakhale mfumu yathuʼ+ aja ali kuti? Abweretseni kuno tiwaphe.”
12 Kenako anthu anauza Samueli kuti: “Amene ankanena kuti, ‘Sauli sangakhale mfumu yathuʼ+ aja ali kuti? Abweretseni kuno tiwaphe.”