Salimo 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzaimbira Yehova chifukwa wandipatsa mphoto yaikulu.+ Luka 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno Mariya ananena kuti: “Moyo wanga ukulemekeza Yehova,*+