1 Samueli 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene Samueli ankapereka nsembe yopsereza, Afilisiti anali akuyandikira kuti amenyane ndi Isiraeli. Zitatero, Yehova anachititsa mabingu amphamvu kwambiri+ pa tsiku limenelo kuti asokoneze+ Afilisiti. Choncho Afilisitiwo anagonjetsedwa ndi Aisiraeli.+ 2 Samueli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova ali kumwamba anayamba kugunda ngati mabingu;+Wamʼmwambamwamba anachititsa kuti mawu ake amveke.+ Salimo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yehova anayamba kugunda ngati mabingu ali kumwamba.+Wamʼmwambamwamba anachititsa kuti mawu ake amveke,+Ndipo kunagwa matalala ndi makala a moto.
10 Pamene Samueli ankapereka nsembe yopsereza, Afilisiti anali akuyandikira kuti amenyane ndi Isiraeli. Zitatero, Yehova anachititsa mabingu amphamvu kwambiri+ pa tsiku limenelo kuti asokoneze+ Afilisiti. Choncho Afilisitiwo anagonjetsedwa ndi Aisiraeli.+
14 Kenako Yehova ali kumwamba anayamba kugunda ngati mabingu;+Wamʼmwambamwamba anachititsa kuti mawu ake amveke.+
13 Kenako Yehova anayamba kugunda ngati mabingu ali kumwamba.+Wamʼmwambamwamba anachititsa kuti mawu ake amveke,+Ndipo kunagwa matalala ndi makala a moto.