1 Mafumu 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndiyeno wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ mutenti+ nʼkudzoza Solomo.+ Zitatero anthuwo anayamba kuliza lipenga nʼkumafuula kuti: “Mfumu Solomo akhale ndi moyo wautali!”
39 Ndiyeno wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ mutenti+ nʼkudzoza Solomo.+ Zitatero anthuwo anayamba kuliza lipenga nʼkumafuula kuti: “Mfumu Solomo akhale ndi moyo wautali!”