Rute 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Azimayi okhala naye pafupi anamupatsa mwanayo dzina lakuti Obedi. Ndipo iwo anati: “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Obedi+ anali bambo ake a Jese,+ yemwe anabereka Davide. 1 Mbiri 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Boazi anabereka Obedi, Obedi anabereka Jese,+
17 Azimayi okhala naye pafupi anamupatsa mwanayo dzina lakuti Obedi. Ndipo iwo anati: “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Obedi+ anali bambo ake a Jese,+ yemwe anabereka Davide.