-
1 Samueli 22:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako Sauli anauza asilikali othamanga amene anali atamuzungulira kuti: “Iphani ansembe a Yehova chifukwa ali kumbali ya Davide! Iwo ankadziwa kuti Davide akuthawa, koma sanandiuze!” Komabe atumiki a mfumuwo sanafune kupha ansembe a Yehova.
-