1 Samueli 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nʼchifukwa chiyani anthu inu mukunyoza nsembe zanga zimene ndinalamula kuti ziziperekedwa mʼnyumba yanga?+ Nʼchifukwa chiyani mukulemekezabe ana anu koposa ine podzinenepetsa ndi mbali zabwino kwambiri za nsembe iliyonse ya anthu anga Aisiraeli?+
29 Nʼchifukwa chiyani anthu inu mukunyoza nsembe zanga zimene ndinalamula kuti ziziperekedwa mʼnyumba yanga?+ Nʼchifukwa chiyani mukulemekezabe ana anu koposa ine podzinenepetsa ndi mbali zabwino kwambiri za nsembe iliyonse ya anthu anga Aisiraeli?+