2 Samueli 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide ankavina mozungulira pamaso pa Yehova ndi mphamvu zake zonse. Apa nʼkuti atavala efodi wansalu.+
14 Davide ankavina mozungulira pamaso pa Yehova ndi mphamvu zake zonse. Apa nʼkuti atavala efodi wansalu.+