1 Samueli 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Davide anayamba kufunsa asilikali amene anali naye pafupi kuti: “Kodi munthu amene angaphe Mfilisitiyu nʼkuchititsa kuti Aisiraeli asiye kunyozedwa amupatsa chiyani? Kodi Mfilisiti wosadulidwa ameneyu ndi ndani kuti azinyoza asilikali a Mulungu wamoyo?”+ 1 Samueli 17:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ine mtumiki wanu ndinapha zilombo ziwiri zonsezi, mkango komanso chimbalangondo. Mfilisiti wosadulidwayu akhalanso ngati chimodzi mwa zilombo zimenezi, chifukwa wanyoza asilikali a Mulungu wamoyo.”+ 2 Samueli 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Davide anatumiza uthenga kwa Isi-boseti+ mwana wa Sauli wakuti: “Ndipatse mkazi wanga Mikala, amene ndinamuperekera malowolo a makungu okwana 100 a Afilisiti, amene amachotsa pochita mdulidwe.”+
26 Davide anayamba kufunsa asilikali amene anali naye pafupi kuti: “Kodi munthu amene angaphe Mfilisitiyu nʼkuchititsa kuti Aisiraeli asiye kunyozedwa amupatsa chiyani? Kodi Mfilisiti wosadulidwa ameneyu ndi ndani kuti azinyoza asilikali a Mulungu wamoyo?”+
36 Ine mtumiki wanu ndinapha zilombo ziwiri zonsezi, mkango komanso chimbalangondo. Mfilisiti wosadulidwayu akhalanso ngati chimodzi mwa zilombo zimenezi, chifukwa wanyoza asilikali a Mulungu wamoyo.”+
14 Kenako Davide anatumiza uthenga kwa Isi-boseti+ mwana wa Sauli wakuti: “Ndipatse mkazi wanga Mikala, amene ndinamuperekera malowolo a makungu okwana 100 a Afilisiti, amene amachotsa pochita mdulidwe.”+