1 Samueli 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Davide anathawa kuchoka ku Nayoti, ku Rama. Koma anapita kwa Yonatani nʼkumuuza kuti: “Kodi ine ndatani?+ Ndalakwa chiyani, ndipo bambo ako ndawalakwira chiyani kuti azifuna kundipha?”
20 Ndiyeno Davide anathawa kuchoka ku Nayoti, ku Rama. Koma anapita kwa Yonatani nʼkumuuza kuti: “Kodi ine ndatani?+ Ndalakwa chiyani, ndipo bambo ako ndawalakwira chiyani kuti azifuna kundipha?”