Ekisodo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake chakopa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito magalasi odziyangʼanira* a azimayi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asamadetse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka kwa Yehova nsembe zowotcha pamoto, zomwe ndi chakudya cha Mulungu wawo, choncho azikhala oyera.+
8 Kenako anapanga beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake chakopa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito magalasi odziyangʼanira* a azimayi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.
6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asamadetse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka kwa Yehova nsembe zowotcha pamoto, zomwe ndi chakudya cha Mulungu wawo, choncho azikhala oyera.+