-
1 Samueli 10:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Anthu onse amene ankamudziwa atamuona akulosera pamodzi ndi aneneri, anayamba kufunsana kuti: “Kodi mwana wa Kisiyu watani? Kodi Sauli nayenso ndi mneneri?”
-