Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Zitatero, Yehova anakwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi si paja Aroni+ Mlevi uja ndi mʼbale wako? Ndikudziwa kuti amalankhula bwino kwambiri. Ndiponso, iye ali mʼnjira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+

  • Ekisodo 4:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu kukachingamira Mose.”+ Choncho Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ ndipo anamulonjera nʼkumukisa.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena